achinyamata

ZIMENE ACHINYAMATA AMAFUNSA

Kodi Ndingatani Kuti Ndisamasinthesinthe Mmene Ndimamvera?

Anthu ambiri amasinthasintha mmene akumvera, koma zimenezi zimasokoneza ana ambiri. Koma chosangalatsa n’choti utha kudziwa bwino zimene zikukuchitikira komanso n’zotheka kupirira vutoli.

MAVIDIYO AMAKATUNI

Kodi Mumakonda Kusewera Magemu a Pakompyuta?

Kusewera magemu a pakompyuta kungakhale kosangalatsa koma kulinso ndi mavuto ake. Kodi mungatani kuti mupewe mavuto ake n’kumachita zinthu zopindulitsadi?

Tasintha mayina a anthu amene tawatchula pa mbali imeneyi