Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri

Kodi Phunziro la Baibulo lomwe a Mboni za Yehova Amachititsa Limakhala Lotani?

Mukamaphunzira Baibulo kwaulere ndi a Mboni za Yehova, mungagwiritse ntchito Baibulo lililonse limene mukufuna. Mungapemphenso onse a m’banja lanu kapena mnzanu wina aliyense kuti akhale nanu pa phunzirolo.

Kodi Ndalama Zoyendetsera Ntchito ya a Mboni za Yehova Zimachokera Kuti?

Dziwani mmene ntchito yolalikira padziko lonse ikuyendera bwino popanda kupemphetsa ndalama kapena kupereka chakhumi.

N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Sakondwerera Masiku Akubadwa?

Onani mfundo 4 zosonyeza chifukwa chimene Mulungu sasangalala ndi zikondwerero zamasiku akubadwa.

Kodi a Mboni za Yehova Amakhulupirira Zotani?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mwachidule zinthu 15 zokhudza zikhulupiriro zathu.

Kodi a Mboni za Yehova Amakhulupirira Yesu?

Dziwani chifukwa chake kukhulupirira Yesu n’kofunika kwambiri kwa Akhristu oona.

Kodi a Mboni za Yehova Amakhulupirira Kuti Chipembedzo Cholondola N’chawo Chokha?

Kodi Yesu anati pali misewu yambiri yopita kumoyo wosatha?

Kodi a Mboni za Yehova Amakhulupirira Kuti Ndiwo Okha Amene Adzapulumuke?

Baibulo limafotokoza za anthu amene angakhale ndi mwayi wodzapulumuka

Kodi a Mboni za Yehova Amalemekeza Zipembedzo Zina?

Dziwani chifukwa chake Akhristu oona amadziwika ndi kulemekeza ena.

N’chifukwa Chiyani Mumakana Kuikidwa Magazi?

Anthu ambiri amaganiza zinthu zosiyanasiyana zolakwika pa nkhani ya zifukwa zimene a Mboni za Yehova amakanira kuikidwa magazi. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zoona zake.

Kodi a Mboni za Yehova Amaona Kuti N’kulakwa Kulandira Katemera?

Mfundo ziwiri za m’Baibulo zingatithandize kusankha pa nkhani yolandira katemera kapena ayi.

Kodi Mumakhulupirira Kuti Dziko Linalengedwa M’masiku 6 Enieni?

Kodi mumadziwa kuti zinthu zina zokhudza chikhulupiriro chakuti Mulungu analenga dziko lapansili masiku 6 enieni zimasemphana ndi zimene Baibulo limanena?

Kodi a Mboni za Yehova Amaona Bwanji Sayansi?

Kodi zimene a Mboni amakhulupirira ndi zogwirizana ndi zimene a sayansi apeza?

Kodi a Mboni za Yehova Amakhulupirira Chipangano Chakale?

Kodi mbali zina za Baibulo ndi zotha ntchito? Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mbiri yakale yofunika kwambiri komanso malangizo othandiza amene Akhristu angaphunzire m’Malemba Achiheberi.

N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Anasintha Zinthu Zina Zomwe Ankakhulupirira?

Sitiyenera kudabwa zinthu zina zikasintha. Atumiki a Mulungu akale ankafunikanso kusintha zinthu zina zomwe poyamba ankazikhulupirira.

N’chifukwa Chiyani Simugwiritsa Ntchito Mtanda Polambira?

Ngakhale kuti ndife Akhristu, sitigwiritsa ntchito mtanda polambira. N’chifukwa chiyani zili choncho?

Kodi a Mboni za Yehova Amapanga Mapemphero Pamodzi ndi Azipembedzo Zina?

Amatsatira mfundo ziti za m’Baibulo poyankha funsoli?

Kodi a Mboni za Yehova Amagwiritsa Ntchito Bwanji Ndalama Zimene Anthu Amapereka?

Kodi a Mboni amagwiritsa ntchito ndalamazi kuti apeze chuma?

Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?

Werengani kuti mudziwe mmene timapezera chiwerengero cha Mboni za Yehova.

Kodi Ndani Anayambitsa Chipembedzo cha Mboni za Yehova?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake tikunena kuti Charles Taze Russell si amene anayambitsa chipembedzo cha Mboni za Yehova.

Kodi Ndalama Zoyendetsera Ntchito ya a Mboni za Yehova Zimachokera Kuti?

Dziwani mmene ntchito yolalikira padziko lonse ikuyendera bwino popanda kupemphetsa ndalama kapena kupereka chakhumi.

Kodi a Mboni za Yehova Amapereka Chakhumi?

Kodi pali chiwerengero chinachake cha ndalama zimene munthu aliyense wa Mboni za Yehova amafunika kupereka?

Kodi a Mboni za Yehova Ali ndi Abusa Amene Amalipidwa?

Kodi mumpingo wa Mboni za Yehova muli anthu ena apamwamba monga abusa? Nanga ndani amene amagwira ntchito yolalikira?

Kodi Akazi a Chipembedzo cha Mboni za Yehova Amalalikira?

Kodi akazi amathandiza bwanji pa ntchito yolalikira imene a Mboni za Yehova akuigwira padziko lonse?

Kodi Mipingo ya Mboni za Yehova Imayendetsedwa Bwanji?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene mipingo yathu imalandirira malangizo.

Kodi Bungwe Lolamulira la Mboni za Yehova Limachita Zotani?

Kodi a m’Bungwe Lolamulira ndi atsogoleri a gulu lathu?

Kodi Bungwe la Watch Tower Bible and Tract Society Ndi Chiyani?

Kodi a Mboni za Yehova amagwiritsa ntchito bwanji bungweli?

N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Sayankha Nkhani Zina Zomwe Anthu Amawanena?

A Mboni za Yehova akamanenezedwa amayesetsa kutsatira mfundo za m’Baibulo, zomwe zimawathandiza kuzindikira “Nthawi yokhala chete ndi nthawi yolankhula.”​—Mlaliki 3:7.

N’chifukwa Chiyani Mumalalikira Kunyumba ndi Nyumba?

Dziwani zimene Yesu anauza ophunzira ake oyambirira kuti azichita.

Kodi Amboni za Yehova Amaganiza Kuti Adzapulumuka mwa Kulalikira Kunyumba ndi Nyumba?

Onani zimene timakhulupira pa nkhani ya mpulumuka ndiponso mmene munthu angapulumukire.

N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Amalalikira Anthu Amene Ali Kale ndi Chipembedzo Chawo?

N’chiyani chimatichititsa kulalikira anthu amene ali kale ndi chipembedzo chawo?

Kodi a Mboni za Yehova Amakakamiza Anthu Kuti Asinthe Zipembedzo Zawo?

Kodi a Mboni za Yehova amalalikira n’cholinga chokopa anthu? Kodi iwo amakakamiza anthu kuti alowe chipembedzo chawo?

Kodi Phunziro la Baibulo lomwe a Mboni za Yehova Amachititsa Limakhala Lotani?

Mukamaphunzira Baibulo kwaulere ndi a Mboni za Yehova, mungagwiritse ntchito Baibulo lililonse limene mukufuna. Mungapemphenso onse a m’banja lanu kapena mnzanu wina aliyense kuti akhale nanu pa phunzirolo.

Kodi a Mboni za Yehova Ali ndi Amishonale?

Kodi ndi anthu otani amene amagwira nawo ntchito ya umishonale, ndipo n’chifukwa chiyani amagwira ntchito imeneyi? Kodi anthu ena amaphunzitsidwa mwapadera kuti azigwira ntchitoyi?

Kodi Akazi a Chipembedzo cha Mboni za Yehova Amalalikira?

Kodi akazi amathandiza bwanji pa ntchito yolalikira imene a Mboni za Yehova akuigwira padziko lonse?

N’chifukwa Chiyani Malo Anu Opempherera Mumawatchula Kuti Nyumba ya Ufumu?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe kumene mawu akuti “Nyumba ya Ufumu ya Mboni za Yehova” anachokera komanso chifukwa chake timawagwiritsa ntchito.

N’chifukwa Chiyani Simugwiritsa Ntchito Mtanda Polambira?

Ngakhale kuti ndife Akhristu, sitigwiritsa ntchito mtanda polambira. N’chifukwa chiyani zili choncho?

N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Mumachita Mwambo wa Mgonero wa Ambuye Mosiyana ndi Zipembedzo Zina?

A Mboni za Yehova amaona kuti Mgonero wa Ambuye kapena kuti Chikumbutso cha Imfa ya Khristu ndi mwambo wopatulika kwambiri. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene Baibulo limanena zokhudza mwambowu.

Kodi a Mboni za Yehova Amapanga Mapemphero Pamodzi ndi Azipembedzo Zina?

Amatsatira mfundo ziti za m’Baibulo poyankha funsoli?

Kodi a Mboni za Yehova Ali ndi Baibulo Lawolawo?

Kugwiritsira ntchito Mabaibulo osiyanasiyana kungakuthandizeni pophunzira Baibulo. Pali zifukwa zitatu zimene zimapangitsa kuti Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika likhale labwino kuphunzira.

Kodi Baibulo la Dziko Latsopano Linamasuliridwa Molondola?

N’chifukwa chiyani Baibulo la Dziko Latsopano limasiyana ndi Mabaibulo ena?

Kodi a Mboni za Yehova Amakhulupirira Chipangano Chakale?

Kodi mbali zina za Baibulo ndi zotha ntchito? Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mbiri yakale yofunika kwambiri komanso malangizo othandiza amene Akhristu angaphunzire m’Malemba Achiheberi.

N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Salowerera Ndale?

Kodi iwo amasokoneza mtendere m’dziko?

N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Sapita Kunkhondo?

A Mboni za Yehova ndi odziwika bwino padziko lonse kuti amakana kupita kunkhondo. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake sitipita kunkhondo.

Kodi a Mboni za Yehova Amagwira Nawo Ntchito Yothandiza Ena Pakagwa Tsoka?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene timachita pothandiza a Mboni anzathu amene akhudzidwa ndi tsoka komanso anthu ena omwe si a Mboni.

Kodi Mumalandira Chithandizo cha Kuchipatala?

Anthu ena amaganiza kuti a Mboni za Yehova amakana chithandizo chilichonse cha mankhwala. Kodi n’zoonadi kuti iwo amakana?

Kodi a Mboni za Yehova Amaona Kuti N’kulakwa Kulandira Katemera?

Mfundo ziwiri za m’Baibulo zingatithandize kusankha pa nkhani yolandira katemera kapena ayi.

N’chifukwa Chiyani Mumakana Kuikidwa Magazi?

Anthu ambiri amaganiza zinthu zosiyanasiyana zolakwika pa nkhani ya zifukwa zimene a Mboni za Yehova amakanira kuikidwa magazi. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zoona zake.

Kodi a Mboni za Yehova Amaiona Bwanji Nkhani ya Maphunziro?

Kodi ndi mfundo ziti zomwe a Mboni za Yehova amaganizira akafuna kusankha maphunziro owonjezera?

Kodi a Mboni za Yehova Amakakamiza Ana Awo Kuti Akhalenso a Mboni?

Mofanana ndi makolo ambiri, nawonso a Mboni za Yehova amafunira ana awo zabwino. Choncho amawaphunzitsa zinthu zomwe zingawathandize.

Kodi a Mboni za Yehova Amapangitsa Kuti Mabanja a Anthu Athe Kapena Alimbe?

Nthawi zina a Mboni za Yehova amanenedwa kuti amapangitsa kuti mabanja a anthu athe. Koma kodi zimenezi n’zoona?

Kodi a Mboni za Yehova Amatsatira Mfundo Ziti Zokhudza Kukhala pa Chibwenzi?

Kodi ndi bwino kukhala pa chibwenzi pongofuna kusangalala?

Kodi a Mboni za Yehova Amaiona Bwanji Nkhani Yothetsa Banja?

Kodi a Mboni za Yehova amathandiza mabanja amene akukumana ndi mavuto? Kodi akulu ayenera kuvomereza ngati wa Mboni akufuna kuthetsa banja?

Kodi a Mboni za Yehova Ali ndi Lamulo Loletsa Mavidiyo Ena, Mabuku Ena Ndiponso Nyimbo Zina?

Kodi Mkhristu ayenera kuganizira mfundo ziti akafuna kusankha zosangalatsa?

N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Sachita Nawo Maholide Ena?

Werengani nkhaniyi kuti mupeze mayankho a mafunso atatu ofunika okhudza mmene a Mboni za Yehova amaonera maholide.

N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Sakondwerera Khirisimasi?

Anthu ambiri amakondwererabe Khirisimasi ngakhale kuti amadziwa chiyambi chake. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe chifukwa chake a Mboni za Yehova sakondwerera Khirisimasi.

N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Sakondwerera Isitala?

Anthu ambiri amaganiza kuti chikondwerero cha Isitala n’chogwirizana ndi Chikhristu. N’chifukwa chiyani a Mboni za Yehova sakondwerera nawo?

N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Sakondwerera Masiku Akubadwa?

Onani mfundo 4 zosonyeza chifukwa chimene Mulungu sasangalala ndi zikondwerero zamasiku akubadwa.

Kodi Paukwati wa Mboni za Yehova Pamachitika Zotani?

Zochitika zina zikhoza kusiyana koma timayendera mfundo zofanana.

N’chifukwa Chiyani a Mboni za Yehova Mumachita Mwambo wa Mgonero wa Ambuye Mosiyana ndi Zipembedzo Zina?

A Mboni za Yehova amaona kuti Mgonero wa Ambuye kapena kuti Chikumbutso cha Imfa ya Khristu ndi mwambo wopatulika kwambiri. Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene Baibulo limanena zokhudza mwambowu.

Kodi a Mboni za Yehova Amakhulupirira Zotani pa Nkhani ya Mwambo wa Maliro?

A Mboni za Yehova amachita miyambo ya maliro motsatira zimene amakhulupirira. Ndiye kodi amatsatira mfundo ziti?

Kodi a Mboni za Yehova Ndi Akhristu?

Onani chifukwa chake timasiyana ndi zipembedzo zina zimene zimati n’zachikhristu.

Kodi Chipembedzo cha Mboni za Yehova ndi cha Chipulotesitanti?

Mfundo ziwiri zimene zimasiyanitsa Mboni za Yehova ndi zipembedzo zina zomwe zimatchedwanso zachikhristu ngakhale kuti si za Chikatolika.

Kodi a Mboni za Yehova Ndi Gulu Lampatuko la ku America?

Onani mfundo zinayi zokhudza gulu limeneli lapadziko lonse.

Kodi a Mboni za Yehova Ndi Gulu la Ziyoni?

Zinthu zimene timakhulupirira zimachokera m’Malemba ndipo Mulungu saona kuti mtundu wina wa anthu ndi wapamwamba kuposa unzake.

Kodi a Mboni za Yehova Ndi Gulu la Mpatuko?

Yerekezerani zinthu ziwiri zimene anthu ambiri amaganiza akamva mawu akuti mpatuko ndi zoona zake zokhudza Mboni za Yehova

Kodi a Mboni za Yehova Alipo Angati Padziko Lonse?

Werengani kuti mudziwe mmene timapezera chiwerengero cha Mboni za Yehova.

Kodi Ndingatani Kuti Ndikhale wa Mboni za Yehova?

Lemba la Mateyu 28:19, 20 limafotokoza zinthu zitatu zimene munthu angachite.

Kodi a Mboni Amafuna Kuti Ndikamaphunzira Nawo Baibulo Nanenso Ndikhale wa Mboni?

A Mboni za Yehova akuphunzira Baibulo ndi anthu mamiliyoni ambiri padziko lonse kwaulere. Koma kodi mukamaphunzira Baibulo ndi ife ndiye kuti nanunso mukhala wa Mboni?

Kodi Munthu Atafuna Angasiye Kukhala wa Mboni za Yehova?

Pali njira ziwiri zimene munthu angagwiritse ntchito kuti zimenezi zitheke.

Kodi a Mboni za Yehova Amapewa Anthu Amene Anatuluka M’chipembedzochi?

Nthawi zina zimakhala zoyenerera kuti munthu achotsedwe mumpingo ndipo zimenezi zimathandiza kuti munthuyo asinthe n’kubwereranso mumpingo.