Pitani ku nkhani yake

Mtendere Komanso Moyo Wosangalala

Tikakumana ndi mavuto aakulu tingayambe kuganiza kuti n’zosatheka kukhala osangalala komanso kukhala ndi mtendere wamumtima. Komatu Baibulo lathandiza anthu ambirimbiri kupirira mavuto omwe amakumana nawo tsiku ndi tsiku. Lawathandizanso kuchepetsako nkhawa komanso kuthana ndi mavuto ena ndipo lawathandiza kuona kuti moyo uli ndi cholinga. Inunso Baibulo lingakuthandizeni kuti muzisangalala.

NKHANI ZINA

Mungatani Kuti Musayambe Kumwa Mowa Mopitirira Malire?

Mfundo 5 zimene zingakuthandizeni kuti musamamwe mowa mopitirira malire ngakhale pamene muli ndi nkhawa kwambiri.

NKHANI ZINA

Mungatani Kuti Musayambe Kumwa Mowa Mopitirira Malire?

Mfundo 5 zimene zingakuthandizeni kuti musamamwe mowa mopitirira malire ngakhale pamene muli ndi nkhawa kwambiri.

Kupirira Mavuto Aakulu

Moyo Wanthanzi

Kukhala Bwino Ndi Anthu

Baibulo Limasintha Anthu

Anthu azikhalidwe zosiyanasiyana asiya makhalidwe awo oipa ndipo ali pa ubwenzi wabwino ndi Mulungu.

Pamene Munthu Amene Mumakonda Amwalira

Kodi mnzanu kapena m’bale wanu anamwalira ndipo mukufunikira kulimbikitsidwa?

Banja Lanu Likhoza Kukhala Losangalala

Mukhoza kukhala ndi banja losangalala mukamatsatira mfundo za m’Baibulo.

Kuphunzira Baibulo ndi Mboni za Yehova

N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo—Vidiyo Yathunthu

Baibulo likuthandiza anthu ambirimbiri padziko lonse lapansi kupeza mayankho a mafunso ofunika kwambiri. Kodi inunso mungakonde?

Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji?

A Mboni za Yehova padziko lonse lapansi amadziwika bwino chifukwa cha ntchito yawo yophunzitsa anthu Baibulo kwaulere. Onani mmene amaphunzitsira.

Pemphani Kuti Tidzakuyendereni

Mutha kukhala ndi mwayi wokambirana nkhani inayake ya m’Baibulo kapena kudziwa zambiri zokhudza Mboni za Yehova.