MAVIDIYO AMAKATUNI

N’chifukwa Chiyani Muyenera Kukhala Oona Mtima?

N’chifukwa Chiyani Muyenera Kukhala Oona Mtima?

Munthu akangoyamba kunama, zimavuta kuti asiye. Phunzirani zokhudza mavuto omwe amakhalapo chifukwa chochita zinthu mwachinyengo komanso ubwino wochita zinthu moona mtima.