Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOTI ACHINYAMATA ACHITE

ZOTI MUCHITE

Musamapitirire Malire

Tsambali likuthandizani kuti muzipewa kutumiza mameseji amene angapangitse munthu wina kuganiza kuti mukufuna akhale chibwenzi chanu.

Kodi N’kungocheza Kapena Kukopana?

Nkhani imene munthu wina angaione ngati yocheza, wina angaione ngati yomukopa. Mungatani kuti muzipewa kutumiza mameseji olakwika?

Zomwe Zingakuthandize Kuti Usamayembekezere Kuchita Zinthu Mosalakwitsa Chilichonse

Zoti muchitezi zikuthandizani kukhala ndi maganizo oyenera a zimene anthu ena komanso inuyo mungakwanitse kuchita.

Zimene Zingakuthandizeni Kuphunzira Chinenero China

Kuphunzira chinenero china kumafunika kuyeserera, nthawi ndi khama. Zoti muchitezi zikuthandizani kudziwa zoyenera kuchita pophunzira chinenero china.