Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOTI MUCHITE POPHUNZIRA BAIBULO

Zoti Muchite Pophunzira Baibulo

Pewani Kulakalaka Zinthu Zoipa

Werengani nkhani ya Davide ndi Bati-seba kuti muone zimene mungaphunzirepo. Koperani nkhaniyi, iwerengeni m’Baibulo, ndipo muiganizire mozama n’kuona mmene ingakuthandizireni.

Muzilandira Uphungu Modzichepetsa

Kodi mungaphunzirepo chiyani mukaganizira mmene Natani anaperekera uphungu kwa Davide?

Pirirani Mavuto Mosangalala

Onani zimene zinathandiza Paulo ndi Sila kuti azisangalalabe ngakhale kuti ankazunzidwa.

Pewani Mtima Wodzikuza

Abisalomu, yemwe anali mwana wa Mfumu Davide, ankafuna kulanda ufumu wa bambo ake. Koma mtima wake wodzikuzawu unam’chititsa kuti ataye moyo wake.