Mabaibulo
Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika ndi lolondola ndiponso losavuta kuwerenga. 307 253,794,253 Kuti mudziwe zambiri zokhudza Baibuloli, onani nkhani yamutu wakuti “Kodi a Mboni za Yehova Ali ndi Baibulo Lawolawo?” komanso “Kodi Baibulo la Dziko Latsopano Linamasuliridwa Molondola?”
M’zilankhulo zina, tinapatsidwa chilolezo choti tifalitse Mabaibulo ena amene amagwiritsidwa ntchito kwambiri m’zilankhulozo.