Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

NTCHITO YOLALIKIRA

Amadutsa Pamchenga wa Pansi pa Nyanja Kupita Kokalalikira

A Mboni za Yehova anapeza njira yowathandiza kuti azikalalikira anthu a patizilumba ta Halligen.

KODI NDANI AKUCHITA CHIFUNIRO CHA YEHOVA MASIKU ANO?

Kodi Timathandiza Bwanji Abale Athu Amene Ali M’mavuto?

Pakachitika tsoka, nthawi yomweyo timayamba kuthandiza abale athu omwe akhudzidwa ndi tsoka powapatsa zinthu zofunika pamoyo komanso timawalimbikitsa mwauzimu. Kodi timachita bwanji zimenezi?

MISONKHANO IKULUIKULU

Tikukuitanani Kuti Mudzakhale Nafe Pamsonkhano wa 2017

Msonkhano wa Mboni za Yehova wa 2017 wa mutu wakuti “Musafooke!” Msonkhanowu udzafotokoza mmene tingakhalire osangalala panopa komanso mmene tingakhalire ndi chiyembekezo chabwino cha m’tsogolo.

MISONKHANO

Misonkhano ya Mpingo ya Mboni za Yehova

Dziwani malo amene a Mboni za Yehova amasonkhana komanso mmene amalambirira Mulungu.

MAFUNSO OFUNSIDWA KAWIRIKAWIRI

Kodi Ndalama Zoyendetsera Ntchito ya a Mboni za Yehova Zimachokera Kuti?

Dziwani mmene ntchito yolalikira padziko lonse ikuyendera bwino popanda kupemphetsa ndalama kapena kupereka chakhumi.

Mfundo Zachidule​—Padziko Lonse

  • 240​—Mayiko amene a Mboni za Yehova amalambira Mulungu

  • 8,340,982​—Mboni za Yehova padziko lonse

  • 10,115,264​—Maphunziro a Baibulo aulere

  • 20,085,142​—Anthu amene anapezeka pa mwambo wokumbukira imfa ya Yesu Khristu

  • 119,485​—Mipingo