Pitani ku nkhani yake

Zimene Mungachite Kuti Mukhale Bambo Wabwino

Malangizo a m’Baibulo awa angathandize mwana wanu kwa moyo wake wonse mukamawagwiritsa ntchito.

 

Onani Zambiri

Werengani Baibulo pa Intaneti

Onani zimene zili mu Baibulo la Dziko Latsopano lomwe ndi lolondola komanso losavuta kuwerenga.

Werengani Baibulo pa Intaneti

Onani zimene zili mu Baibulo la Dziko Latsopano lomwe ndi lolondola komanso losavuta kuwerenga.

Onani mavidiyo, nyimbo ndi nkhani zimene zangoikidwa kumene.

Onani Zatsopano

Yambani kuphunzira Baibulo

Phunzirani Baibulo kwaulere, mochita kukambirana ndi mphunzitsi wanu.

Pemphani Kuti Tidzakuyendereni

Mutha kukhala ndi mwayi wokambirana nkhani inayake ya m’Baibulo kapena kudziwa zambiri zokhudza Mboni za Yehova.

Misonkhano ya Mpingo ya Mboni za Yehova

Dziwani malo amene a Mboni za Yehova amasonkhana komanso mmene amalambirira Mulungu.

Kodi a Mboni za Yehova Mumawadziwa?

Ndife anthu ochokera m’mitundu, zikhalidwe ndiponso zinenero zosiyanasiyana, koma ndife ogwirizana kwambiri chifukwa cholinga chathu n’chimodzi. Cholinga chathu chachikulu n’kulemekeza Yehova, Mulungu wotchulidwa m’Baibulo ndiponso Mlengi wa zinthu zonse. Timayesetsa kutsanzira Yesu Khristu ndipo timanyadira kutchedwa Akhristu. Nthawi zonse aliyense wa ife amathera nthawi yake pothandiza ena kuphunzira Baibulo ndiponso za Ufumu wa Mulungu. Timatchedwa kuti Mboni za Yehova chifukwa choti timachitira umboni, kapena kuti kulalikira za Yehova Mulungu ndi Ufumu wake.

Fufuzani pa Webusaiti yathuyi. Werengani Baibulo pa Intaneti. Dziwani zambiri za ifeyo ndiponso zimene timakhulupirira.

 

Anthu Awiri a Mboni za Yehova Akulalikira Munthu Wina Mmunda wa Mphunga.