Chichewa
Nyimbo za Chikhristu
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1011211/univ/wpub/1011211_univ_sqr_xl.jpg

Nyimbo za Chikhristu

Mvetserani kapena pangani dawunilodi nyimbo za Chikhristu zomwe zimagwiritsidwa ntchito potamanda komanso kulambira Yehova Mulungu. Pakupezeka nyimbo za mawu, zoimbidwa ndi zipangizo zokhazokha komanso manotsi.

NYIMBO ZA BROADCASTING

Tidzawaonanso

Tikaferedwa, chiyembekezo chakuti akufa adzauka chimatilimbikitsa kuti tithe kupirira.

NYIMBO ZA BROADCASTING

Tidzawaonanso

Tikaferedwa, chiyembekezo chakuti akufa adzauka chimatilimbikitsa kuti tithe kupirira.