Chichewa
Pezani a Mboni za Yehova
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1011231/univ/art/1011231_univ_sqr_xl.jpg

Tipezeni

Timasangalala kuthandiza anthu amene akufunitsitsa kuphunzira Baibulo komanso amene akufuna kudziwa zomwe timachita padziko lonse. Sankhani chimodzi mwa zinthu zomwe zili m’munsizi kuti mukumane ndi a Mboni za Yehova m’dera lanu.