Pitani ku nkhani yake

Pemphani Kuti Tidzakuyendereni

Kodi mukufuna kudziwa zambiri zokhudza Baibulo kapena a Mboni za Yehova? Ngati ndi choncho, pemphani kuti wa Mboni za Yehova wina adzakuyendereni polemba fomu ili m’munsimu ndipo Wamboni wa m’dera lanu adzalankhula nanu.

Tidzagwiritsa ntchito zomwe mudzatumizezo poyankha pempho lanu ndipo sitidzazigwiritsa ntchito pa zinthu zina. Zimenezi n’zogwirizana ndi mfundo zathu zonena za Zinthu Zokhudza Munthu (Global Policy on Use of Personal Data).

Tidzakuimbirani Foni

Mukalemba ndi kutitumizira fomu, pasanathe wiki imodzi kapena mawiki awiri, wa Mboni za Yehova wina adzakuimbirani foni.

Phunzirani Baibulo

Phunzirani zomwe Baibulo limaphunzitsa pa nkhani zosiyanasiyana kapena pemphani kuti tiziphunzira nanu Baibulo mochita kukambirana.

Potengera Zomwe Mungakonde

Mukhoza kumaphunzira pamasom’pamaso kapena pogwiritsa ntchito zipangizo zamakono, panthawi ndi malo omwe mungakonde.

Chidziwitso Chokhudza Matenda a Kolonavairasi (COVID-19): M’madera ambiri tasiya kaye kukumana ndi anthu pamasom’pamaso. Mukamalemba fomuyi, chonde ikani nambala yanu ya foni ndipo wa Mboni wa m’dera lanu adzakuimbirani.