Mfundo Zothandiza Akuluakulu a Boma Komanso Atolankhani

M’chigawo ichi muli mfundo zolondola zokhudza Mboni za Yehova, zomwe ndi zothandiza kwa akuluakulu a boma komanso atolankhani.

Zokhudza Mboni za Yehova Potengera Dziko

A Mboni za Yehova Anamangidwa Chifukwa cha Zimene Amakhulupirira​—Potengera Dera

Madera amene a Mboni za Yehova anamangidwa, ndipo nthawi zina amazunzidwa kwambiri, chifukwa cha zimene amakhulupirira ngakhale kuti umenewu ndi ufulu wawo.

Mawu Amene a Mboni za Yehova Amagwiritsa Ntchito Komanso Kalembedwe Kake

Malangizo ovomerezeka othandiza atolankhani kuti azigwiritsa ntchito bwino mawu komanso kuwalemba molondola pofotokoza zokhudza chipembedzo chathu.