Timapepala ndi Zoitanira
Timapepala tathu tili ndi uthenga wachidule wokhudza nkhani inayake ya m’Baibulo. Timapepala toitanira anthu kumisonkhano yathu yampingo komanso ikuluikulu tilinso patsamba lomweli. Aliyense ndi wolandiridwa ku misonkhano imeneyi.

