Pitani ku nkhani yake

Zokhudza Mboni za Yehova Padziko Lonse

  • Mayiko amene a Mboni za Yehova amalambira Mulungu​—239

  • Mboni za Yehova padziko lonse​—8,686,980

  • Maphunziro a Baibulo aulere​—5,908,167

  • Anthu amene anapezeka pa mwambo wokumbukira imfa ya Yesu Khristu​—21,367,603

  • Mipingo​—119,297

 

Mboni za Yehova Padziko Lonse

Timapezeka padziko lonse ndipo timachokera m’mitundu komanso zikhalidwe zosiyanasiyana. Mwina mukudziwa kuti timagwira ntchito yolalikira koma timagwiranso ntchito zina zothandiza anthu a m’madera athu.

Onaninso

MABUKU

Lipoti la Chaka Chautumiki cha 2021 la Mboni za Yehova Padziko Lonse.

Onani mmene ntchito ya Mboni za Yehova yolalikira padziko lonse inayendera kuyambira mu September 2020 mpaka mu August 2021.

NSANJA YA OLONDA

Kodi a Mboni za Yehova Mumawadziwa Bwinobwino?

Kodi inuyo mumaona a Mboni ngati mmene anthu ena omwe atchulidwa m’nkhaniyi amaganizira?