• Mudzi wa Laura, Majuro Atoll, Marshall Islands​—Akulalikira m’chinenero cha Chimashalizi kwa munthu woumitsa mtedza wa kokonati

Mfundo Zachidule—Marshall Islands

  • 69,747—Chiwerengero cha anthu
  • 226—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 4—Mipingo
  • Pa anthu 309 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi