Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Malangizo Othandiza Banja Lonse

M’banja ndi malo abwino amene anthu angasonyezerane chikondi komanso kulimbikitsana pa mavuto atsiku ndi tsiku. Inuyo mungachite zinthu zothandizira kuti banja lanu lonse likhale losangalala ngati mutamagwiritsa ntchito malangizo a m’Baibulo omwe ndi othandiza. Dziwani izi: Tasintha maina ena otchulidwa m’nkhani yakuti, “Anthu Apabanja Ndiponso Makolo” komanso “Achinyamata.”

 

Mabanja ndi Makolo

Kodi Baibulo Limaloleza Kuthetsa Ukwati?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene Mulungu amaloleza komanso zimene amadana nazo.

Kodi Mungatani Kuti Mukhale Makolo Abwino?

Kodi mungatani kuti ana anu akule bwino?

Achinyamata

Kodi Ndingafotokoze Bwanji Zimene Ndimakhulupirira pa Nkhani ya Kugonana?

Ngati mutafunsidwa kuti: ‘Kodi sunagonanepo ndi munthu chibadwire?’ kodi mungathe kugwiritsa ntchito Baibulo poyankha?

Kodi Ndi Mnzanga Chabe Kapena Amandifuna?—Gawo 2: Kodi Ndikumukopa?

Kodi mnzanuyu angaganize kuti mukumufuna chibwenzi? Zimene zingakuthandizeni.

Ana

Mwana wa Mchemwali wake wa Paulo Anali Wolimba Mtima

Zimene anachitazo zinapulumutsa moyo wa ankolo ake. Kodi mukudziwa zimene anachita?

Timoteyo Ankafuna Kuthandiza Anthu

Kodi iweyo ungatani kuti ukhale ndi moyo wosangalala ngati Timoteyo?