Achibale
Zimene Mungachite Kuti Muzigwirizana ndi Achibale
N’zotheka kulemekeza makolo anu popanda kusokoneza banja lanu.
Mungatani Kuti Muzigwirizana Ndi Apongozi Anu?
Mfundo zitatu zomwe zingakuthandizeni kuti nkhani zokhudza apongozi zisasokoneze banja lanu.
Kodi Baibulo Limanena Zotani pa Nkhani Yosamalira Makolo Achikulire?
Baibulo limafotokoza zimene amuna ndi akazi ena anachita m’mbuyomo posamalira makolo awo achikulire. Lilinso ndi mfundo zomwe zingathandize anthu omwe akusamalira makolo achikulire panopa.
Kodi Munthu Angasonyeze Bwanji Kuti ‘Amalemekeza Bambo Ake ndi Mayi Ake’?
Mukhoza kudabwa kudziwa zimene lamuloli silitanthauza.
Mungatani Ngati Munthu Amene Mumamukonda Akudwala Matenda Oti Sachira?
Kodi achibale angalimbikitse komanso kusamalira bwanji munthu amene akudwala matenda oti sachira? Kodi achibale angatani kuti asavutike kwambiri pa nthawi imene m’bale wawoyo akudwala?
Zimene Banja la Ana Opeza Lingachite Kuti Lizigwirizana ndi Anthu Ena
Kodi mfundo za m’Baibulo zingathandize bwanji makolo a m’banja la ana opeza kuti azigwirizana ndi anzawo, achibale komanso makolo enieni a anawo?

