Pitani ku nkhani yake

Kupeza Komanso Kukhala pa Chibwenzi

Kodi Ndi Mnzanga Chabe Kapena Amandifuna?​—Gawo 1: Kodi Ndikuona Zizindikiro Zotani?

Nkhaniyi ingakuthandizeni kuti mudziwe ngati munthu amakukondani kapena akungofuna kukhala mnzanu chabe.

Kodi Ndi Mnzanga Chabe Kapena Amandifuna?—Gawo 2: Kodi Ndikumukopa?

Kodi mnzanuyu angaganize kuti mukumufuna chibwenzi? Zimene zingakuthandizeni.

Kodi Ndi Chikondi Chenicheni Kapena Kungotengeka Maganizo?

Onerani vidiyoyi kuti mudziwe tanthauzo la kutengeka maganizo ndiponso chikondi chenicheni.

Kodi Kukopana Kuli Ndi Vuto?

Kodi kukopana n’kutani? N’chifukwa chiyani anthu ena amakopana? Kodi kukopana kuli ndi vuto?

Chikondi Chenicheni

Mfundo za m’Baibulo zingathandize Akhristu posankha munthu woyenera kumanga naye banja, ndiponso zingawathandize kusonyezana chikondi chenicheni akakwatirana.

Kodi Ndafika Poti N’kukhala ndi Chibwenzi?

Onani mafunso 4 amene angakuthandizeni kudziwa ngati mwafika poti n’kukhala ndi chibwenzi.

Kodi Ndafika Poti N’kulowa M’banja?

Kuti muyankhe funso limeneli, muyenera kudzidziwa bwino nokha. Onani mafunso amene angakuthandizeni kudzidziwa bwino.

Kodi Munthu Ameneyu Ndi Woyenera Kuti Ndimange Naye Banja?

Kodi n’chiyani chimene chingakuthandizeni kuti mudziwe makhalidwe enieni a mnzanuyo?

Kodi a Mboni za Yehova Amatsatira Mfundo Ziti Zokhudza Kukhala pa Chibwenzi?

Kodi ndi bwino kukhala pa chibwenzi pongofuna kusangalala?

Kodi Ndithetse Chibwenzichi?—Gawo 1

Mukalowa m’banja, mukuyenera kukhala ndi mnzanuyo kwa moyo wanu wonse. Ndiye ngati mukuona kuti munthu amene muli naye pachibwenzi sangakhale woyenera kumanga naye banja, musangokhala osachitapo chilichonse.

Kodi Ndithetse Chibwenzichi?—Gawo 2

Kuthetsa chibwenzi si chinthu chophweka. Koma kodi mungatani kuti muthetse chibwenzi m’njira yabwino?

Kodi Mungatani Ngati Chibwenzi Chatha?

N’chiyani chingakuthandizeni ngati chibwenzi chanu chatha?