Pitani ku nkhani yake

Zokuthandizani za pa Intaneti

Laibulale ya JW ya Chinenero Chamanja

Gwiritsani ntchito pulogalamu yathu yapazipangizo za m’manja kuti mupange dawunilodi, kusunga komanso kuonera Baibulo komanso mabuku ndi zinthu zina za m’chinenero chamanja.

Kuphunzira Chinenero pa JW

Pulogalamu yothandiza pophunzira chineneroyi, ili ndi magawo othandiza polalikira anthu m’zinenero zosiyanasiyana. Magawowa ndi monga mawu ojambulidwa a chinenero chimene mukuphunzira komanso kudziwa tanthauzo la mawu a chinenero china.