Zatsopano pa JW.ORG

2024-05-22

KHALANI MASO

N’chifukwa Chiyani Makhalidwe Abwino Alowa Pansi?—Kodi Baibulo Limanena Zotani?

Makhalidwe abwino alowa pansi kwambiri panopa. Baibulo limafotokoza chifukwa chake makhalidwe abwino alowa pansi komanso lili ndi malangizo omwe angathandize anthu kukhala ndi makhalidwe abwino.

2024-05-22

ANTHU OKWATIRANA KOMANSO MABANJA

Kodi Tiyambe Kukhala Limodzi Tisanakwatirane?

Anthu ena amaganiza kuti kuyamba kukhala limodzi kaye asanakwatirane kungawathandize kukonzekera banja. Kodi amenewa ndi maganizo abwino kapena pali njira ina yabwino?

2024-05-22

ANTHU OKWATIRANA KOMANSO MABANJA

Mungatani Kuti Mupewe Kuthetsa Banja Pambuyo Pokhala Limodzi kwa Zaka Zambiri?

N’chiyani chikuchititsa kuti anthu azithetsa banja pambuyo pokhala limodzi kwa zaka zambiri? Kodi mungatani kuti zimenezi zisakuchitikireni?

2024-05-20

NYIMBO ZA BROADCASTING

“M’dziko Labwino”

Kuganizira kwambiri za chiyembekezo chathu kumatithandiza kupirira ngakhale mavuto aakulu.

2024-05-01

NSANJA YA OLONDA

Kodi Tingapeze Kuti Malangizo Otithandiza Kusankha Zinthu Mwanzeru?

Phunzirani mmene mungasankhire zinthu mwanzeru zomwe zingadzathandize inuyo ndi banja lanu.

2024-05-01

NKHANI ZINA

Kuteteza Akazi—Zimene Baibulo Limanena

Mulungu amaona kuti akazi ayenera kutetezedwa. Onani chifukwa chake amaona choncho komanso zimene adzachite pothetsa nkhanza zonse zimene anthu amachitira akazi.