JW Library Sign Language
JW Library Sign Language, ndi pulogalamu yovomerezeka ya Mboni za Yehova. Pulogalamuyi imatha kupanga dawunilodi, kuika mavidiyo a chinenero chamanja m’malo oyenera ndi kuwaonetsa pa jw.org.
Mukhoza kuika JW Library Sign Language Pachipangizo cha Android popanda kupita ku App Store
Ngati zikukuvutani kuika JW Library Sign Language pa chipangizo chanu cha Android kudzera ku Google Play Store kapena Amazon Appstore, mukhoza kuika nokha pogwiritsa ntchito JW Library Sign Language Android Package Kit (APK)
Mafunso Ofunsidwa Kawirikawiri—JW Library Sign Language
Pezani mayankho a mafunso ofunsidwa kawirikawiri.