Pitani ku nkhani yake

Laibulale

Palaibulaleyi mungapezepo mabuku, magazini, mavidiyo ndi zinthu zina zothandiza pophunzira Baibulo. Werengani komanso kuchita dawunilodi magazini atsopano a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! komanso zinthu zina zomwe zasonyezedwa m’munsimu. Mvetserani kwaulere nkhani za m’mabuku ndi magazini athu zomwe zinajambulidwa m’zinenero zambiri. Onerani komanso kuchita dawunilodi mavidiyo m’zinenero zambiri komanso a m’chinenero chamanja.

 

NSANJA YA OLONDA

Kodi N’zotheka Kuthetsa Chidani?

Kodi n’chiyani chimene chikufunika kuti makhalidwe omwe amayambitsa chidani monga kusalana, kuchitirana zachipongwe, nkhanza komanso kuphana zitheretu?

NSANJA YA OLONDA

Kodi N’zotheka Kuthetsa Chidani?

Kodi n’chiyani chimene chikufunika kuti makhalidwe omwe amayambitsa chidani monga kusalana, kuchitirana zachipongwe, nkhanza komanso kuphana zitheretu?

Magazini

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

GALAMUKANI!

NSANJA YA OLONDA

Mabuku ndiponso Timabuku

Nthawi zina zimene tingasinthe m’mabuku komanso zinthu zina zoikidwa pawebusaitiyi sitingazisinthe mwamsanga m'mabuku ochita kusindikiza.

Zinthu Zina Zokuthandizani

JW Library

Werengani ndi kuphunzira Baibulo pogwiritsa ntchito Baibulo la Dziko Latsopano. Yerekezerani zimene Mabaibulo ena amanena.

Laibulale ya pa Intaneti (opens new window)

Fufuzani nkhani za m'Baibulo pa Intaneti m'mabuku a Mboni za Yehova.