NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA) July 2024

M’magaziniyi muli nkhani zophunzira kuyambira September 9–​October 6, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 27

Muzikhala Olimba Mtima Ngati Zadoki

Idzaphunziridwa mlungu woyambira September 9-15, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 28

Kodi Mumatha Kuzindikira Choonadi?

Idzaphunziridwa mlungu woyambira September 16-22, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 29

Tiyenera Kukhala Maso Kuti Tizipewa Mayesero

Idzaphunziridwa mlungu woyambira September 23-29, 2024.

NKHANI YOPHUNZIRA 30

Zimene Tikuphunzira kwa Mafumu a Chiisiraeli

Idzaphunziridwa mlungu woyambira September 30–​October 6, 2024.

Kodi Mungatani Kuti Muzolowere Mukasamukira Mumpingo Wina?

Akhristu ambiri zimawayendera bwino akasamukira mumpingo watsopano. Kodi n’chiyani chingakuthandizeni ngati mwasamukira mumpingo wina? Onani mfundo 4 zimene zingakuthandizeni kuti muzolowere msanga mpingo watsopanowo.

Mafunso Ochokera kwa Owerenga

Kodi “mkazi” wotchulidwa pa Yesaya 60:1 ndi ndani, nanga ‘anaimirira’ bwanji komanso anaonetsa bwanji “kuwala”?