Pulogalamu ya Msonkhano Wachigawo wa 2024 Wakuti ‘Lalikirani Uthenga Wabwino’

Lachisanu

Pulogalamu ya lachisanu yachokera pa Luka 2:10​—“Uthenga wabwino wa chimwemwe chachikulu chimene anthu onse adzakhale nacho.”

Loweruka

Pulogalamu ya Loweruka yachokera pa Salimo 96:2​—“Tsiku ndi tsiku muzilengeza uthenga wabwino wa chipulumutso chake.”

Lamlungu

Pulogalamu ya Lamlungu yachokera pa Mateyu 24:14​—“. . . kenako mapeto adzafika.”

Mawu kwa Osonkhana

Mfundo zothandiza amene asonkhana.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

ZOKHUDZA IFEYO

Mudzapezeke nawo Pamsonkhano Wachigawo wa 2024​—’Lalikirani Uthenga Wabwino’

Tikukuitanani kuti mudzakhale nawo pamsonkhano wa Mboni za Yehova wachaka chino wa masiku atatu

MISONKHANO IKULUIKULU

Mukuitanidwa ku Msonkhano wa Mboni za Yehova wa 2024 Wakuti ‘Lalikirani Uthenga Wabwino’

Tikukuitanani kuti mudzakhale nafe pamsonkhano wa Mboni za Yehova wa masiku atatu wachaka chino.

MISONKHANO IKULUIKULU

Zimene Zili Muvidiyo Yakuti: Kuwala Kwenikweni kwa Dziko

Onerani zimene zili muvidiyo yoyamba yakuti Moyo wa Yesu Komanso Utumiki Wake. Vidiyo imeneyi idzaonetsedwa pamsonkhano wa 2024.