Chichewa
Chikondi Chenicheni
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1102012819/univ/art/1102012819_univ_sqr_xl.jpg

Chikondi Chenicheni

Chikondi Chenicheni

Liz ndi Magie ankagwirizana kwambiri ndipo onse ankafuna atapeza chikondi chenicheni koma aliyense anali ndi maganizo osiyana ndi a mnzake ponena za mmene angachipezere.