Chikondi Chenicheni

Anthu amene amatsatira zimene mabuku ofotokoza za chikondi amanena nthawi zambiri chikondi chawo sichipita patali, koma anthu amene ali ndi chikondi chenicheni amatsatira mfundo za m’Baibulo zomwe sizisintha.

Chikondi Chenicheni

Mfundo za m’Baibulo zingathandize Akhristu posankha munthu woyenera kumanga naye banja, ndiponso zingawathandize kusonyezana chikondi chenicheni akakwatirana.

Chikondi Chenicheni​—Mawu Oyamba

Mukhoza kupindula ndi mfundo za m’vidiyoyi ngakhale kuti padziko lapansi pali miyambo yosiyanasiyana imene anthu amatsatira akakhala pa chibwenzi.