• Mzinda wa Zurich, m’dziko la Switzerland​—Akulalikira uthenga wa m’Baibulo pogwiritsa ntchito tizikwangani ta m’manja

  • Mzinda wa Montreux, m’dziko la Switzerland​—Akugawira kabuku kofotokoza Baibulo pafupi ndi nyumba yakale yotchedwa Château de Chillon

  • Lucerne, Switzerland​—Akuonetsa kavidiyo ka pa jw.org

  • Lavaux region, Switzerland—Kulalikira uthenga wa m’Baibulo

Mfundo Zachidule—Switzerland

  • 8,482,152—Chiwerengero cha anthu
  • 19,354—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 272—Mipingo
  • Pa anthu 438 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi