Pitani ku nkhani yake

  • Southern Iceland​—Akulalikira mlimi pogwiritsa ntchito buku la Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni?, la m’chinenero cha Chiayisilandi

Mfundo Zachidule—Iceland

  • 335,679—Chiwerengero cha anthu
  • 377—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 7—Mipingo
  • Pa anthu 890 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi