• Dublin, Ireland​—Akugawira kapepala kakuti Kodi Mukufuna Kudziwa Choonadi? kumalo otchedwa Grand Canal Square

GALAMUKANI!

Dziko la Ireland

Werengani zokhudza anthu ansangala a ku Emerald Isle.

NTCHITO YOLALIKIRA

Kulalikira M’dera Lakutali M’dziko la Ireland

Banja likufotokoza mmene ntchito yolalikira ku Ireland, yawathandizira kukhala ogwirizana.

ZOCHITIKA ZAPADERA

Msonkhano Wapadera ku Ireland

A Mboni za Yehova ku Dublin m’dziko la Ireland, analandira alendo ochokera m’mayiko ena amene anabwera ku Msonkhano Wapadera wa mu 2012, umene unali ndi mutu wakuti ‘Tetezani Mtima Wanu!’ Onani zimene ena ananena zokhudza msonkhano umenewu.