• Gael’, Yap, Micronesia​—Akugawira kabuku kofotokoza nkhani za m’Babulo pamalo osungira ndalama zakale za miyala

Mfundo Zachidule—Yap

  • 11,376—Chiwerengero cha anthu
  • 30—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 1—Mipingo
  • Pa anthu 379 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi