• Bishkek, Kyrgyzstan​—Akuonetsa vidiyo ya chinenero cha Chirikigizi yakuti, N’Chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo?

GALAMUKANI!

Dziko la Kyrgyzstan

Anthu a ku Kyrgyzstan ndi ochereza komanso aulemu. Kodi amatsatira miyambo yanji yokhudza banja?