• Dera lotchedwa Hallstatt ku Austria​—Akulalikira nyumba ndi nyumba

  • Vienna, Austria—Akulalikira ku Michaelerplatz

  • Ku Vienna m’dziko la Austria​—Akugawira mabuku ofotokoza Baibulo pa malo otchedwa Maria-Theresien-Platz

Mfundo Zachidule—Austria

  • 8,823,054—Chiwerengero cha anthu
  • 21,563—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 299—Mipingo
  • Pa anthu 409 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi