Mfundo Zachidule—Botswana
- 2,360,000—Chiwerengero cha anthu
- 2,543—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 45—Mipingo
- Pa anthu 961 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NTCHITO YOLALIKIRA
Pachionetsero cha ku Botswana Panali Chuma Chamtengo Wapatali
Ana omwe anafika pamalowa anachita chidwi kwambiri ndi mavidiyo a makatuni a mutu wakuti Khalani Bwenzi la Yehova omwe amathandiza anthu kugwiritsa ntchito mfundo za m’Baibulo.

