• Dyer Bay, Maine, United States—Akuphunzitsa pogwiritsa ntchito Baibulo

  • Dera la Tallahassee ku Florida m’dziko la United States​—Akumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani?

  • Dyer Bay, Maine, United States—Akuphunzitsa pogwiritsa ntchito Baibulo

  • Dera la Tallahassee ku Florida m’dziko la United States​—Akumuonetsa vidiyo yakuti Kodi pa Nyumba ya Ufumu Pamachitika Zotani?

NTCHITO ZOMANGAMANGA

Anzathu Atsopano ku Warwick

Akuluakulu a tawuni ya Warwick ndi enanso akufotokoza zinthu zabwino zimene zakhala zikuchitika pamene ankagwira ntchito ndi a Mboni za Yehova pomanga likulu lawo latsopano.

NTCHITO ZOMANGAMANGA

Anthu Omwe si Mboni Anasangalala Kugwira Ntchito Ndi Mboni za Yehova ku Warwick

Kodi ogwira ntchito komanso madalaivala omwe si a Mboni ananena zotani atagwira ntchito ndi a Mboni pa ntchito yomanga?

Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2017

“Ndinu Aneba Abwino”

Pa May 7 ndi 8, 2016, anthu anaona malo ku Brooklyn Heights, New York ndipo izi zinathandiza kuti anthuwa adziwe zokhudza Beteli ya ku Brooklyn.

Buku Lapachaka la Mboni za Yehova la 2017

Zimene Zachitika M’chaka Chapitachi

Malipotiwa akusonyeza zimene a Mboni za Yehova padziko lonse achita posonyeza kuti amakhulupirira Mulungu, amachita zabwino komanso amayesetsa kukhala okhulupirika.—Salimo 37:3.

NTCHITO YOLALIKIRA

Anthu Oyambirira Kukhala ku America Anachita Chikondwerero ku New York

Pachikondwerero cha ku New York mu 2015, anthu ambiri anachita chidwi ndi mabuku amene a Mboni za Yehova anabweretsa omwe anali m’zilankhulo za anthu oyambirira kukhala ku America.

MOYO WA PA BETELI

Chionetsero Chapadera cha Baibulo

Kuyambira kale, Yehova Mulungu wakhala akuuza anthu dzina lake. Onerani vidiyoyi kuti mudziwe zimene omasulira Baibulo achita pofuna kuti dzina la Mulungu lisaiwalike.

ZOCHITIKA ZAPADERA

Akuluakulu a Mzinda wa Atlanta Analandira a Mboni za Yehova ndi Manja Awiri

Akuluakulu a mzinda analandira anthu ochokera m’mayiko 28 omwe ankadzachita msonkhano mumzindawu. Misonkhano itatu inachitikira mumzindawu mwezi wa July ndi wa August 2014.

MOYO WA PA BETELI

Tikukuitanani Kuti Mudzaone Maofesi Athu ku United States

Mudzaonanso Likulu la Padziko Lonse la Mboni za Yehova lomwe lili ku United States.

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku New York

N’chiyani chinachititsa anthu okhala m’nyumba yabwino kwambiri kuti alolere kusamukira m’kanyumba kakang’ono kwambiri

MOYO WA PA BETELI

Ulendo Wosaiwalika

Bambo Marcellus analimbana ndi mavuto ambiri kuti ulendo wawo okaona ofesi ya nthambi ya ku United States ndiponso malikulu apadziko lonse a Mboni za Yehova utheke. Kodi ulendowu unalidi wofunikadi?

NTCHITO ZOMANGAMANGA

Kuteteza Zachilengedwe ku Warwick

A Mboni za Yehova ayamba ntchito yomanga maofesi omwe akhale likulu lawo latsopano la padziko lonse ku New York. Kodi iwo akuchita zotani pofuna kuteteza zachilengedwe?

MOYO WA PA BETELI

Famu Yomwe Ikudyetsa Anthu Mamiliyoni

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mmene malo athu osindikizira mabuku amene ali kufamu ya Watchtower kumpoto kwa dera la New York, akuthandizira anthu mamiliyoni kuti azidya chakudya chauzimu.