• Padoko la Waitemata mumzinda wa Auckland, New Zealand—Akulalikira uthenga wa m’Baibulo kwa msodzi

GALAMUKANI!

Dziko la New Zealand

Ngakhale kuti dziko New Zealand lili kutali kwambiri, alendo pafupifupi 3 miliyoni amalowa m’dzikoli. Kodi n’chiyani chimawachititsa chidwi alendowa?