Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa
  • Corozal, Belize​—Akulalikira kwa munthu amene akugwira ntchito

GALAMUKANI!

Dziko la Belize

Dziko la Belize ndiye loyambirira kukhala ndi malo otetezera nyama za ngati akambuku ndipo ndi dziko lachiwiri lomwe lili ndi zomera za mtundu wa coral reef zazikulu kwambiri.