Mfundo Zachidule—Guatemala
- 18,080,000—Chiwerengero cha anthu
- 39,427—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 780—Mipingo
- Pa anthu 461 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Anaona Chikondi cha Abale ndi Alongo
NKHANI
A Mboni za Yehova ndi Okonzeka Kuyamba Ntchito Yomanganso Nyumba Zoonongeka ndi Chivomezi ku Guatemala ndi ku Mexico
A Mboni za Yehova ayamba ntchito yayikulu yothandiza a Mboni anzawo a ku Mexico ndi ku Guatemala amene anakhudzidwa ndi zivomezi ziwiri zomwe zinaononga kwambiri.

