Mfundo Zachidule—Slovenia
- 2,131,000—Chiwerengero cha anthu
- 1,735—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 22—Mipingo
- Pa anthu 1,244 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi


Trenta Valley, Slovenia—Akugawira kabuku
Ptuj, Slovenia—Akuitanira aneba ku Nyumba ya Ufumu kuti akasonkhane nawo
Trenta Valley, Slovenia—Akugawira kabuku
Ptuj, Slovenia—Akuitanira aneba ku Nyumba ya Ufumu kuti akasonkhane nawo