Mboni za Yehova Padziko Lonse

Uruguay

  • Montevideo, Uruguay​—Akugawira kapepala kakuti, Kodi Mukuganiza Kuti Zinthu Zidzakhala Bwanji M’tsogolo?

Mfundo Zachidule—Uruguay

  • 3,486,000—Chiwerengero cha anthu
  • 12,117—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 148—Mipingo
  • Pa anthu 291 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi