ZOCHITIKA PA MOYO

Anadzipereka ndi Mtima Wonse ku Guyana

Kodi tingaphunzire zotani kwa anthu amene anatumikirapo kumene kukufunika olalikira ambiri? Kodi zimene iwo ananena zingakuthandizeni bwanji kukonzekera kukatumikira kudziko lina ngati mukufuna kutero?