• Paramaribo, Suriname—Akukambirana nkhani ya m’Baibulo pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu.

Mfundo Zachidule—Suriname

  • 569,874—Chiwerengero cha anthu
  • 3,133—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 56—Mipingo
  • Pa anthu 182 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi