Mboni za Yehova Padziko Lonse

Congo (Kinshasa)

Mfundo Zachidule—Congo (Kinshasa)

  • 115,685,000—Chiwerengero cha anthu
  • 306,303—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 4,810—Mipingo
  • Pa anthu 389 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?

Sitinaiwale Abale ndi Alongo Athu Powathandiza Pangozi Zogwa Mwadzidzidzi mu 2021

M’chaka cha 2021, m’mayiko ena anthu ankafunika kuthandizidwa chifukwa cha mliri wa COVID-19 komanso ngozi zikuluzikulu zam’chilengedwe.

NKHANI

A Mboni za Yehova Anapereka Chithandizo kwa Anthu Othawa Nkhondo ku Congo

A Mboni za Yehova akupereka chithandizo kwa Akhristu anzawo komanso anthu ena omwe anathawa nkhondo m’chigawo cha Kasai ku Democratic Republic of the Congo.

NTCHITO YOFALITSA MABUKU

Ntchito Yotumiza Mabuku ku Congo

A Mboni za Yehova amayenda mtunda wautali mwezi uliwonse kuti akasiye Mabaibulo ndiponso mabuku kwa anthu a m’dziko la Congo.