BUKU LAPACHAKA LA MBONI ZA YEHOVA LA 2014

Sierra Leone ndi Guinea

Nkhaniyi ikusonyeza kuti Mboni za Yehova zakhala zikulalikira uthenga wabwino m’mayiko awiriwa mokhulupirika komanso modzipereka kwambiri.