• Trakai Island Castle, Lithuania​—Akugawira kabuku ka Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu m’chinenero cha Chilituweniya

Mfundo Zachidule—Lithuania

  • 2,799,127—Chiwerengero cha anthu
  • 3,026—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 46—Mipingo
  • Pa anthu 925 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi