• Tel Aviv, Israel—Akulalikira m’kanjira mu chinenero cha Chirasha

ZOCHITIKA ZAPADERA

Msonkhano Wapadera ku Israel

Mgwirizano wochititsa chidwi wa anthu ochokera m’mayiko osiyanasiyana unaonekera mu 2012 ku Tel Aviv, m’dziko limene kwa zaka zambiri, anthu akhala akudana chifukwa chosiyana mitundu ndi zipembedzo.