Mboni za Yehova Padziko Lonse

Venezuela

  • La Victoria, Venezuela​—Akuphunzitsa ena Baibulo panyumba yawo kwa ulele

Mfundo Zachidule—Venezuela

  • 28,517,000—Chiwerengero cha anthu
  • 139,199—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 1,726—Mipingo
  • Pa anthu 206 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi

KODI ZOPEREKA ZANU ZIMAGWIRITSIDWA NTCHITO BWANJI?

Sitinaiwale Abale ndi Alongo Athu Powathandiza Pangozi Zogwa Mwadzidzidzi mu 2021

M’chaka cha 2021, m’mayiko ena anthu ankafunika kuthandizidwa chifukwa cha mliri wa COVID-19 komanso ngozi zikuluzikulu zam’chilengedwe.

NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)

Ndimadalira Yehova Posankha Zochita

Mbiri ya Moyo Wanga: Dyah Yazbek

NKHANI

Mmene Zinthu Zilili Panopa ku Venezuela: Ntchito ya a Mboni za Yehova Ikupitabe Patsogolo Ngakhale Kuti Mavuto Sakutha

Ngakhale kuti zinthu zafika poipa, a Mboni za Yehova ku Venezuela akupitiriza kugwira ntchito yolalikira molimba mtima.