Mboni za Yehova Padziko Lonse

Aruba

  • Ku San Nicolas, ku Aruba (mu January 1950). M’bale Henry Tweed ndi mkazi wawo Alice amene anali amishonale, ataima limodzi ndi Mlongo Oris Mills kutsogolo kwa Nyumba ya Ufumu yoyamba ku Aruba. Patapita nthawi, Mlongo Mills ndi mwamuna wawo Woodworth Mills, anatumikira kwa zaka zambiri monga amishonale ku Nigeria komanso ku St. Lucia

  • Rodgers Beach, ku Aruba​—Akugawira kabuku kakuti Mungakhale ndi Moyo Mpaka Kalekale

  • Rodgers Beach, ku Aruba​—Akuonetsa vidiyo yakuti Kodi Phunziro la Baibulo Limachitika Bwanji?

  • Rodgers Beach, ku Aruba​—Akulalikira uthenga wa m’Baibulo wopatsa chiyembekezo

Mfundo Zachidule—Aruba

  • 108,000—Chiwerengero cha anthu
  • 1,106—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 13—Mipingo
  • Pa anthu 99 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi