Pitani ku nkhani yake

  • M’chigawo cha Kunene, ku Namibia​—Akulalikira anthu a mtundu wa Chihimba pogwiritsa ntchito kabuku kakuti Mverani Mulungu Kuti Mudzapeze Moyo Wosatha, m’chinenero cha Chiherero

Mfundo Zachidule—Namibia

  • 2,579,051—Chiwerengero cha anthu
  • 2,473—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
  • 45—Mipingo
  • Pa anthu 1,043 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi