Mfundo Zachidule—Saint Maarten
- 44,000—Chiwerengero cha anthu
- 329—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 4—Mipingo
- Pa anthu 141 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NKHANI
A Mboni Akugwira Mwakhama Ntchito Yothandiza Anthu Omwe Anakhudzidwa Ndi Mphepo Zamkuntho
Maofesi a Nthambi a Mboni za Yehova akufotokoza zimene akuchita pothandiza komanso kutonthoza mwauzimu anthu okhudzidwa ndi mphepo yamkuntho ya Irma ndi Maria.

